1 Samueli 17:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nthawi yomweyo, Davide anasiya katundu wake kwa munthu amene ankasamalira katundu, ndipo anathamangira kumalo omenyera nkhondo. Atafika, anayamba kufunsa ngati azichimwene ake ali bwino.+
22 Nthawi yomweyo, Davide anasiya katundu wake kwa munthu amene ankasamalira katundu, ndipo anathamangira kumalo omenyera nkhondo. Atafika, anayamba kufunsa ngati azichimwene ake ali bwino.+