1 Samueli 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Asilikali onse a Isiraeli ataona Goliyati, anachita mantha kwambiri ndipo anayamba kuthawa.+