Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 17:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndiyeno asilikali a Isiraeli anayamba kunena kuti: “Mukumuona munthu akubwera apoyo? Iye amabwera kudzanyoza Aisiraeli.+ Munthu amene angamenyane naye nʼkumupha, mfumu idzamʼpatsa chuma chochuluka komanso mwana wake wamkazi.+ Kuwonjezera pamenepo, nyumba ya bambo ake a munthuyo idzasiya kupereka zinthu zimene Aisiraeli ayenera kupereka kwa mfumu.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena