Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 17:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Eliyabu+ mchimwene wake wamkulu wa Davide atamva Davideyo akulankhula ndi anthuwo, anapsa naye mtima kwambiri. Iye anati: “Wabwera kudzatani kuno? Nanga nkhosa zochepa zija wasiyira ndani kuchipululu?+ Ine ndikudziwa bwino kuti ndiwe wodzikuza komanso uli ndi maganizo olakwika. Iweyo wabwera kuno kuti udzaone mmene nkhondo ikuyendera.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena