1 Samueli 17:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Atatero, anachokapo nʼkupita kwa munthu wina ndipo anafunsanso funso lomwe lija.+ Anthu anamuyankhanso chimodzimodzi ngati poyamba paja.+
30 Atatero, anachokapo nʼkupita kwa munthu wina ndipo anafunsanso funso lomwe lija.+ Anthu anamuyankhanso chimodzimodzi ngati poyamba paja.+