1 Samueli 17:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Davide anauza Sauli kuti: “Aliyense asachite naye mantha.* Ine mtumiki wanu ndipita kukamenyana naye Mfilisiti ameneyu.”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:32 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 5 2016, tsatsa. 10-11
32 Davide anauza Sauli kuti: “Aliyense asachite naye mantha.* Ine mtumiki wanu ndipita kukamenyana naye Mfilisiti ameneyu.”+