1 Samueli 17:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma Sauli anauza Davide kuti: “Sungapite kukamenyana ndi Mfilisiti ameneyu chifukwa ndiwe mwana.+ Mfilisitiyu wakhala akumenya nkhondo kuyambira ali mnyamata.” 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:33 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 5 2016, tsa. 11
33 Koma Sauli anauza Davide kuti: “Sungapite kukamenyana ndi Mfilisiti ameneyu chifukwa ndiwe mwana.+ Mfilisitiyu wakhala akumenya nkhondo kuyambira ali mnyamata.”