1 Samueli 17:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Davide anauza Sauli kuti: “Ine mtumiki wanu ndinakhala mʼbusa wa nkhosa za bambo anga. Ndiyeno kunabwera mkango+ komanso chimbalangondo ndipo chilombo chilichonse chinagwira nkhosa. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:34 Nsanja ya Olonda,9/1/2011, tsa. 27
34 Davide anauza Sauli kuti: “Ine mtumiki wanu ndinakhala mʼbusa wa nkhosa za bambo anga. Ndiyeno kunabwera mkango+ komanso chimbalangondo ndipo chilombo chilichonse chinagwira nkhosa.