1 Samueli 17:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zitatero, ndinatsatira chilombocho nʼkuchimenya, ndipo ndinapulumutsa nkhosa mʼkamwa mwake. Chitayamba kundilusira ndinachikoka ubweya* nʼkuchipha. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:35 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 5 2016, tsatsa. 9-10 Nsanja ya Olonda,9/1/2011, tsa. 27
35 Zitatero, ndinatsatira chilombocho nʼkuchimenya, ndipo ndinapulumutsa nkhosa mʼkamwa mwake. Chitayamba kundilusira ndinachikoka ubweya* nʼkuchipha.