1 Samueli 17:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ine mtumiki wanu ndinapha zilombo ziwiri zonsezi, mkango komanso chimbalangondo. Mfilisiti wosadulidwayu akhalanso ngati chimodzi mwa zilombo zimenezi, chifukwa wanyoza asilikali a Mulungu wamoyo.”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:36 Nsanja ya Olonda,7/15/1993, tsa. 25
36 Ine mtumiki wanu ndinapha zilombo ziwiri zonsezi, mkango komanso chimbalangondo. Mfilisiti wosadulidwayu akhalanso ngati chimodzi mwa zilombo zimenezi, chifukwa wanyoza asilikali a Mulungu wamoyo.”+