1 Samueli 17:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Davide anawonjezera kuti: “Yehova amene anandipulumutsa mʼkamwa mwa mkango ndi mʼkamwa mwa chimbalangondo andipulumutsanso mʼmanja mwa Mfilisiti ameneyu.”+ Sauli anauza Davide kuti: “Pita, ndipo Yehova akhale nawe.” 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:37 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 5 2016, tsa. 11
37 Davide anawonjezera kuti: “Yehova amene anandipulumutsa mʼkamwa mwa mkango ndi mʼkamwa mwa chimbalangondo andipulumutsanso mʼmanja mwa Mfilisiti ameneyu.”+ Sauli anauza Davide kuti: “Pita, ndipo Yehova akhale nawe.”