-
1 Samueli 17:39Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
39 Kenako Davide anamangirira lupanga pazovala zake. Koma atanyamuka kuti azipita, analephera kuyenda chifukwa zovalazo sanazizolowere. Davide anauza Sauli kuti: “Sinditha kuyenda nazo zovala zimenezi chifukwa sindinazizolowere.” Atatero, Davide anavula zovalazo.
-