1 Samueli 17:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndiyeno anatenga ndodo mʼmanja mwake nʼkusankha miyala 5 yosalala yakumtsinje.* Iye anaika miyalayi mʼchikwama chake cha kubusa ndipo ananyamulanso gulaye*+ mʼmanja mwake. Kenako anayamba kupita kumene kunali Mfilisiti uja. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:40 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 5 2016, tsa. 11
40 Ndiyeno anatenga ndodo mʼmanja mwake nʼkusankha miyala 5 yosalala yakumtsinje.* Iye anaika miyalayi mʼchikwama chake cha kubusa ndipo ananyamulanso gulaye*+ mʼmanja mwake. Kenako anayamba kupita kumene kunali Mfilisiti uja.