1 Samueli 17:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Choncho iye anafunsa Davide kuti: “Kodi ine ndine galu+ kuti ubwere kwa ine ndi ndodo?” Atatero, anatemberera Davide mʼdzina la milungu yake. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:43 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 5 2016, tsa. 11
43 Choncho iye anafunsa Davide kuti: “Kodi ine ndine galu+ kuti ubwere kwa ine ndi ndodo?” Atatero, anatemberera Davide mʼdzina la milungu yake.