-
1 Samueli 17:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 Iye anauzanso Davide kuti: “Tangoyerekeza kubwera kuno, ndipereka mnofu wako kwa mbalame zamumlengalenga ndi kwa zilombo zakutchire.”
-