-
1 Samueli 17:48Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
48 Mfilisiti uja anayamba kupita kumene kunali Davide. Nayenso Davide anayamba kuthamanga mofulumira kupita kumalo omenyera nkhondo kuti akakumane naye.
-