1 Samueli 17:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Davide anapisa dzanja mʼchikwama chake nʼkutenga mwala. Kenako anauponya ndi gulaye moti unamenya Mfilisiti uja pamphumi nʼkuloweratu mʼmutu mwake, ndipo anagwa pansi chafufumimba.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:49 Nsanja ya Olonda (Yogawira),No. 5 2016, tsa. 12 Nsanja ya Olonda,1/1/1989, ptsa. 19, 21
49 Davide anapisa dzanja mʼchikwama chake nʼkutenga mwala. Kenako anauponya ndi gulaye moti unamenya Mfilisiti uja pamphumi nʼkuloweratu mʼmutu mwake, ndipo anagwa pansi chafufumimba.+