1 Samueli 17:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Choncho Davide anagonjetsa Mfilisitiyo pogwiritsa ntchito gulaye ndi mwala. Iye anamugwetsa nʼkumupha ngakhale kuti Davide analibe lupanga mʼmanja mwake.+
50 Choncho Davide anagonjetsa Mfilisitiyo pogwiritsa ntchito gulaye ndi mwala. Iye anamugwetsa nʼkumupha ngakhale kuti Davide analibe lupanga mʼmanja mwake.+