1 Samueli 17:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Pa nthawi imene Davide ankapita kukakumana ndi Mfilisiti uja, Sauli anafunsa Abineri,+ mkulu wa asilikali, kuti: “Abineri, kodi ameneyu ndi mwana wa ndani?”+ Abineri anayankha kuti: “Ndithu mfumu muli apa,* ine sindikudziwa.” 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:55 Nsanja ya Olonda,3/15/2005, ptsa. 23-24
55 Pa nthawi imene Davide ankapita kukakumana ndi Mfilisiti uja, Sauli anafunsa Abineri,+ mkulu wa asilikali, kuti: “Abineri, kodi ameneyu ndi mwana wa ndani?”+ Abineri anayankha kuti: “Ndithu mfumu muli apa,* ine sindikudziwa.”