1 Samueli 17:58 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 Ndiyeno Sauli anamufunsa kuti: “Mnyamata iwe, kodi bambo ako ndi ndani?” Davide anayankha kuti: “Ndine mwana wa mtumiki wanu Jese,+ wa ku Betelehemu.”+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:58 Nsanja ya Olonda,8/15/2007, tsa. 198/1/2007, tsa. 31
58 Ndiyeno Sauli anamufunsa kuti: “Mnyamata iwe, kodi bambo ako ndi ndani?” Davide anayankha kuti: “Ndine mwana wa mtumiki wanu Jese,+ wa ku Betelehemu.”+