-
1 Samueli 18:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Ndiyeno Yonatani anavula mkanjo wake wodula manja nʼkumupatsa Davide. Anamupatsanso zovala zake zankhondo, lupanga, uta ndi lamba.
-