1 Samueli 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Davide anayamba kupita kunkhondo ndipo kulikonse kumene Sauli wamutumiza, zinthu zinkamuyendera bwino.+ Choncho Sauli anamuika kuti akhale mkulu wa asilikali+ ndipo zimenezi zinasangalatsa anthu onse komanso atumiki a Sauli. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:5 Nsanja ya Olonda,3/15/1989, tsa. 12
5 Davide anayamba kupita kunkhondo ndipo kulikonse kumene Sauli wamutumiza, zinthu zinkamuyendera bwino.+ Choncho Sauli anamuika kuti akhale mkulu wa asilikali+ ndipo zimenezi zinasangalatsa anthu onse komanso atumiki a Sauli.