1 Samueli 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Sauli anakwiya kwambiri+ ndipo nyimbo imeneyi inkamunyasa, moti anayamba kuganiza kuti: “Akutamanda Davide ponena kuti wapha masauzande ambirimbiri, koma ine akunena kuti ndapha masauzande okha. Ndiye kuti kwatsala nʼkumupatsa ufumuwutu basi!”+
8 Sauli anakwiya kwambiri+ ndipo nyimbo imeneyi inkamunyasa, moti anayamba kuganiza kuti: “Akutamanda Davide ponena kuti wapha masauzande ambirimbiri, koma ine akunena kuti ndapha masauzande okha. Ndiye kuti kwatsala nʼkumupatsa ufumuwutu basi!”+