1 Samueli 18:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Sauli anaponya mkondowo+ ndipo mumtima mwake ankati: ‘Ndibaya Davide nʼkumukhomerera kukhoma!’ Koma Davide anazinda nʼkuthawa ndipo zimenezi zinachitika kawiri konse. 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:11 Nsanja ya Olonda,9/15/2008, tsa. 4
11 Kenako Sauli anaponya mkondowo+ ndipo mumtima mwake ankati: ‘Ndibaya Davide nʼkumukhomerera kukhoma!’ Koma Davide anazinda nʼkuthawa ndipo zimenezi zinachitika kawiri konse.