1 Samueli 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho Sauli anachotsa Davide kuti asamakhalenso naye pafupi, ndipo anamuika kukhala mtsogoleri wa gulu la asilikali 1,000, moti Davide ankatsogolera asilikali kunkhondo.+
13 Choncho Sauli anachotsa Davide kuti asamakhalenso naye pafupi, ndipo anamuika kukhala mtsogoleri wa gulu la asilikali 1,000, moti Davide ankatsogolera asilikali kunkhondo.+