1 Samueli 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Mikala+ mwana wamkazi wa Sauli ankakonda Davide. Anthu anauza Sauli za nkhaniyi ndipo Sauli atamva anasangalala.
20 Ndiyeno Mikala+ mwana wamkazi wa Sauli ankakonda Davide. Anthu anauza Sauli za nkhaniyi ndipo Sauli atamva anasangalala.