1 Samueli 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho Sauli anati: “Ndimʼpatsa Mikala kuti akhale msampha kwa iye, kuti Afilisiti amuphe.”+ Zitatero Sauli anauzanso Davide kachiwiri kuti: “Lero uchita nane mgwirizano wa ukwati.”*
21 Choncho Sauli anati: “Ndimʼpatsa Mikala kuti akhale msampha kwa iye, kuti Afilisiti amuphe.”+ Zitatero Sauli anauzanso Davide kachiwiri kuti: “Lero uchita nane mgwirizano wa ukwati.”*