1 Samueli 18:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pa nthawi iliyonse imene akalonga a Afilisiti apita kukamenya nkhondo, zinthu zinkamuyendera bwino kwambiri Davide kuposa atumiki onse a Sauli,+ moti dzina la Davide linatchuka kwambiri.+
30 Pa nthawi iliyonse imene akalonga a Afilisiti apita kukamenya nkhondo, zinthu zinkamuyendera bwino kwambiri Davide kuposa atumiki onse a Sauli,+ moti dzina la Davide linatchuka kwambiri.+