1 Samueli 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Sauli anauza mwana wake Yonatani komanso atumiki ake onse kuti akufuna kupha Davide.+