1 Samueli 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Popeza kuti Yonatani, mwana wa Sauli, ankakonda kwambiri Davide,+ iye anauza Davide kuti: “Bambo anga akufuna kukupha. Chonde mawa mʼmawa usamale. Udzapite kukabisala ndipo ukakhale komweko.
2 Popeza kuti Yonatani, mwana wa Sauli, ankakonda kwambiri Davide,+ iye anauza Davide kuti: “Bambo anga akufuna kukupha. Chonde mawa mʼmawa usamale. Udzapite kukabisala ndipo ukakhale komweko.