1 Samueli 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndipita nawo kutchire kumene ukabisaleko ndipo ndikaima pafupi ndi bambo anga. Bambo anga ndikalankhula nawo za iwe, ndipo zilizonse zimene zikachitike, ndidzakuuza ndithu.”+
3 Ine ndipita nawo kutchire kumene ukabisaleko ndipo ndikaima pafupi ndi bambo anga. Bambo anga ndikalankhula nawo za iwe, ndipo zilizonse zimene zikachitike, ndidzakuuza ndithu.”+