1 Samueli 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho Yonatani analankhula zabwino za Davide+ kwa Sauli bambo ake. Iye anawauza kuti: “Mfumu isachimwire mtumiki wake Davide, chifukwa iye sanakulakwireni, ndipo wakhala akukuchitirani zinthu zabwino kwambiri.
4 Choncho Yonatani analankhula zabwino za Davide+ kwa Sauli bambo ake. Iye anawauza kuti: “Mfumu isachimwire mtumiki wake Davide, chifukwa iye sanakulakwireni, ndipo wakhala akukuchitirani zinthu zabwino kwambiri.