1 Samueli 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anaika moyo wake pangozi* nʼkupha Mfilisiti uja,+ moti Yehova anapulumutsa Aisiraeli.* Inuyo munaona zimenezi ndipo munasangalala. Ndiye nʼchifukwa chiyani mukufuna kuchimwira magazi osalakwa, popha Davide popanda chifukwa?”+
5 Iye anaika moyo wake pangozi* nʼkupha Mfilisiti uja,+ moti Yehova anapulumutsa Aisiraeli.* Inuyo munaona zimenezi ndipo munasangalala. Ndiye nʼchifukwa chiyani mukufuna kuchimwira magazi osalakwa, popha Davide popanda chifukwa?”+