-
1 Samueli 19:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Patapita nthawi, nkhondo inayambanso ndipo Davide anapita kukamenyana ndi Afilisiti. Iye anapha Afilisiti ambiri ndipo Afilisiti otsala anagonja nʼkuthawa.
-