1 Samueli 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zitatero Sauli anafunsa Mikala kuti: “Nʼchifukwa chiyani wandipusitsa chonchi nʼkuthawitsa mdani wanga?”+ Mikala anayankha Sauli kuti: “Anandiuza kuti, ‘Ndisiye ndithawe! Apo ayi, ndikupha.’”
17 Zitatero Sauli anafunsa Mikala kuti: “Nʼchifukwa chiyani wandipusitsa chonchi nʼkuthawitsa mdani wanga?”+ Mikala anayankha Sauli kuti: “Anandiuza kuti, ‘Ndisiye ndithawe! Apo ayi, ndikupha.’”