-
1 Samueli 19:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Sauli atauzidwa zimenezi, nthawi yomweyo anatumiza anthu ena, ndipo nawonso anayamba kuchita zinthu ngati aneneri. Zitatero, Sauli anatumiza gulu lina lachitatu, koma nawonso anayamba kuchita zinthu ngati aneneri.
-