1 Samueli 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako nayenso Sauli ananyamuka kupita ku Rama. Atafika pachitsime chachikulu chimene chili ku Seku, anafunsa kuti: “Kodi Samueli ndi Davide ali kuti?” Anthu anayankha kuti: “Ali ku Nayoti,+ ku Rama.”
22 Kenako nayenso Sauli ananyamuka kupita ku Rama. Atafika pachitsime chachikulu chimene chili ku Seku, anafunsa kuti: “Kodi Samueli ndi Davide ali kuti?” Anthu anayankha kuti: “Ali ku Nayoti,+ ku Rama.”