-
1 Samueli 19:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Sauli akupitiriza ulendo wake wopita ku Nayoti, ku Rama, nayenso analandira mzimu wa Mulungu ndipo anayamba kuchita zinthu ngati mneneri mpaka kukafika ku Nayoti, ku Rama.
-