1 Samueli 19:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Sauli nayenso anavula zovala zake, ndipo anayambanso kuchita zinthu ngati mneneri pafupi ndi Samueli. Iye anagona pomwepo ali wosavala* masana onse ndi usiku wonse. Nʼchifukwa chake anthu amanena kuti: “Kodi Sauli nayenso ndi mneneri?”+
24 Sauli nayenso anavula zovala zake, ndipo anayambanso kuchita zinthu ngati mneneri pafupi ndi Samueli. Iye anagona pomwepo ali wosavala* masana onse ndi usiku wonse. Nʼchifukwa chake anthu amanena kuti: “Kodi Sauli nayenso ndi mneneri?”+