1 Samueli 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngati bambo ako angazindikire kuti ine palibe, uwauze kuti, ‘Davide anandichonderera kuti ndimulole kuchoka mwamsanga kuti apite kumzinda wakwawo ku Betelehemu,+ chifukwa banja lawo lonse likukapereka nsembe ya pachaka.’+
6 Ngati bambo ako angazindikire kuti ine palibe, uwauze kuti, ‘Davide anandichonderera kuti ndimulole kuchoka mwamsanga kuti apite kumzinda wakwawo ku Betelehemu,+ chifukwa banja lawo lonse likukapereka nsembe ya pachaka.’+