-
1 Samueli 20:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Ngati anganene kuti, ‘Palibe vuto!’ ndiye kuti zinthu zili bwino kwa ine mtumiki wako. Koma ngati angakwiye, udziwe kuti atsimikiza mtima kundichitira zoipa.
-