1 Samueli 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Undisonyeze chikondi chokhulupirika ine mtumiki wako,+ chifukwa iwe ndi ine tinachita pangano pamaso pa Yehova.+ Koma ngati ndili wolakwa,+ undiphe iweyo, mʼmalo moti ukandipereke kwa bambo ako.”
8 Undisonyeze chikondi chokhulupirika ine mtumiki wako,+ chifukwa iwe ndi ine tinachita pangano pamaso pa Yehova.+ Koma ngati ndili wolakwa,+ undiphe iweyo, mʼmalo moti ukandipereke kwa bambo ako.”