1 Samueli 20:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yonatani anayankha kuti: “Nʼzosatheka kuti iwe ukhale wolakwa! Ngati ndingadziwe zoipa zimene bambo anga akufuna kukuchitira, ukuganiza kuti sindingakuuze?”+
9 Yonatani anayankha kuti: “Nʼzosatheka kuti iwe ukhale wolakwa! Ngati ndingadziwe zoipa zimene bambo anga akufuna kukuchitira, ukuganiza kuti sindingakuuze?”+