1 Samueli 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova andilange ine Yonatani mowirikiza, ndikadziwa kuti bambo anga akufuna kukuchitira zoipa koma osakudziwitsa nʼkukulola kuti upite mwamtendere. Yehova akhale nawe+ ngati mmene anakhalira ndi bambo anga.+
13 Yehova andilange ine Yonatani mowirikiza, ndikadziwa kuti bambo anga akufuna kukuchitira zoipa koma osakudziwitsa nʼkukulola kuti upite mwamtendere. Yehova akhale nawe+ ngati mmene anakhalira ndi bambo anga.+