1 Samueli 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo kodi sudzandisonyeza chikondi chokhulupirika cha Yehova ndili moyo ngakhalenso nditafa?+