1 Samueli 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Usadzasiye kusonyeza anthu amʼbanja langa chikondi chokhulupirika,+ ngakhale pamene Yehova adzawononga mdani aliyense wa Davide padziko lapansi.”
15 Usadzasiye kusonyeza anthu amʼbanja langa chikondi chokhulupirika,+ ngakhale pamene Yehova adzawononga mdani aliyense wa Davide padziko lapansi.”