-
1 Samueli 20:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ndiyeno ndidzauza mtumiki wanga kuti, ‘Pita ukatole miviyo.’ Koma ndikadzauza mtumikiyo kuti, ‘Mivi ili mbali iyo, pita ukatole,’ iweyo ukatuluke chifukwa ndikulumbira mʼdzina la Yehova, Mulungu wamoyo, zinthu zidzakhala kuti zili bwino ndipo palibe chodetsa nkhawa chilichonse.
-