1 Samueli 20:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsiku lotsatira,* mpando wa Davide unakhalabe wopanda munthu. Choncho Sauli anafunsa mwana wake Yonatani kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwana wa Jese+ sanabwere kudzadya dzulo ndi lero?”
27 Tsiku lotsatira,* mpando wa Davide unakhalabe wopanda munthu. Choncho Sauli anafunsa mwana wake Yonatani kuti: “Nʼchifukwa chiyani mwana wa Jese+ sanabwere kudzadya dzulo ndi lero?”