-
1 Samueli 20:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Anandiuza kuti, ‘Chonde ndilole ndipite chifukwa banja lathu likukapereka nsembe mumzinda wakwathu. Mchimwene wanga ndi amene wandiitanitsa. Choncho ngati ungandikomere mtima, ndilole ndipite ndikaone abale anga.’ Nʼchifukwa chake sanabwere kudzadya ndi mfumu.”
-