-
1 Samueli 20:41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
41 Mnyamatayo atapita, Davide anatuluka pamene anabisala, ndipo panali pafupi pompo, chakumʼmwera. Ndiyeno anagwada nʼkuwerama katatu. Atatero, Davide ndi Yonatani anakisana ndipo onse anayamba kulira, koma Davide ndi amene analira kwambiri.
-